First off all.mafuna kuziwitsen kut I have an idea komaso magwira ntchito ntchito ku company ina yake yomwe timagulitsa ma phone zithu zina zama electronics. Nde ineyo maganizo anga anali oti nditapeza ndalama nditha kuyamba kupanga business yanga itha kukhala business yomweyo sinanga ndili nd idea komaso knowledge pa business imeneyi, nde cholinga changa chinali choti nditapeza capital nditha kuyamba kupanga...