ndikufuna kumagula ndikugulitsa chimanga soya komaso mtedza kwathu kuno kuoda chimanga ndi 800 per kg kugulitsa ndi 900 per kg ndi 3 million nditha kupanga phindu locholuka coz ndimapanga business yomweyi koma mpamba wanga ndi 300,000 koma ndimakwanitsa kupezamo ndithu kaphindu nde ndichita mwai wa mpamba business yanga itha kukwera