Kutsegula ma babashop kumayenda muma school kumeta ana pamtengo otsika ngati mbari imodzi yotukulira maphuzilo poonetsetsa kut ana akuoneka bwino kutsegula shop yosoka ma schools uniform ndikumapereka kwa ana a school popanga mgwilizano ndi ma sukulu potolera ndalama koma kupereka pamtengo otsika kwa ana asukulu powalila kumapeleka pang'ono pang'ono