D&P Event Decorators and Sound Systems ndi kampani yochita zokongongoletsa pamalo ndikubwereketsa sound system yomwe tikuiyembekeza kunyambitsa kuno Ku kasungu ,kwa Juma. Ganizo ili lidadza poona kuti anthu ambiri akukumana ndimavuto kuti apeze dekoleshoni yapamwamba yodalilika kuno Ku kasungu moti anthu ena akakhala ndizochitika monga maukwati ndi misonkhano, amachita kuitanitsa dekoleshoni kuchoka madera ena ngati...