•Nkhanga zathu farm, uwu ndi ulimi wankhanga womwe ndakhala ndikuuganizila kwathawi yayitali. •Ulimuwu ndiwabwino komaso ndiwosavuta potengela kuti nkhanga sizimafuna mwankhwala ambiri kuti zikule komaso nkhanga zimatha kuchulukana mwachangu kwambr •Ulimuwoso potengela athu ambiri akufuna protein ochuluka kuchokela munyama ndiye nyama yang'ombe ndiyodula kwambr kutengela nkhanga komaso nkhuku zambr...