Ndikufunitsitsa mtapanga ulimi wa Chimanga ndi nyemba,monga khobwe ndi mitundu ina ya nyemba yosiyanasiyana.ulimiwu ndiopangira kulithipe mbali mwa sinje wa lithipe side Here in Salima.ndicholinga changa kutero ndimafunitsitsa mtapanga ulimiwu koma zithu zimavuta kukwanilitsa chifukwa cha kucepekedwa kwa ndalama pa ulimiwu.timaganyu tomwe ndimapanga sindifikira pa zokhumba zanga za kupanga ulimiwu.Ulimi wu ndidaona...