FASHION STORE 365 ndi bizinesi yomwe ikufuna kutsegula sitolo yamakono ya zovala ku Lilongwe. Pakadali pano bizinesi ikuyenda bwino pa WhatsApp, Facebook ndi ma order a pa phone ndipo ndili ndi makasitomala oposa 40 omwe amabwera mobwerezabwereza. Anthu amakonda katundu wanga chifukwa ndi wapamwamba komanso wotsika mtengo komaso makasitolamala ena ndimakanika ku wafikila chifukwa Amafuna zinthu zambiri zoti ndaodele...