Ng'ombe zoyamba zikhala za nyama kumagulisa zikakula then ma kasitomala azindipeza ..ndekut pakutha kwa chaka zambili zikhala zachitika ...Kmaso ndikhodza kupezaso ziweto zina like mbuz ..nkhuku etc Ng'ombe zachiwiri zikhala za mkaka ..ndekut ndiyesesa kut ndipeze ma kastomala Ku school ..hospital ma office ..kmaso ndilemba anchito kut azindithandiza kut kupanga run business imeneyi