Kugula mbewu zosiyanasiyana kumamidzi ndikumagulisa pa trading center ya PHALOMBE (pa BOMA).. Mbewu Ndi monga nyemba, khobwe, Mtedza, mpunga, mapila, Soya , popcorn, nandolo, chimanga, tchana, ufa komaso kupanga ufa wa phala la soya.. Apa ndifotokozela mene ndingama ndingama odele mbewezo ngakhale mitengo imasithasitha ndiyamba kufotokoza za nyemba.. ndizifotikoza profit yomwe ndingapange nditakhala zoti ndikuyamba...