Business yanga ndikhoza kumagulitsa nkhuku zachizungu ndekut ndikhoza kuyamba kuweta nkhuku zokwana 200, ndalama inayo ndikhoza kugula zipangizo zopangila feed ya nkhuku chifukwa chot feed yogula imakhala yokwelera mtengo kusiyana ndikumapanga wekha,ndikhoza kukhala ndi anyamata azanga awiri othandizana nawo kusamalira nkhuku zanthu ndekut ikamatha ma sabata 6 nkhuku zokwana 200 zija zizakhala zayamba kubweretsa...