Bizinesi yanga Ndikufuna Ndizigulitsa zakudya zomwe banja lililonse limafunikira tsiku ndi tsiku. Ntchito Yanga yaikulu ndi kugulitsa nyemba ndi mpunga wamitundu yosiyanasiyana komanso wabwino kwambiri. Ndizigulitsa m'njira ziwiri kuti tithandize aliyense. Choyamba Ndizigulitsa matumba akulu a 25kg ndi 50kg kwa iwo omwe ali ndi mashopu, malo odyera, ndi mabanja akulu. Kachiwiri Ndizipakira Mutima jumbo...