Dopat Solar Grid ndi kampani yopanga ndikugulitsa magetsi a mphamvu ya zuwa yemwe tikufuna kuyambitsa ku chilumba, karonga. Tizalunjika Madera akumidzi kumene magetsi a Escom sanafike monga Dera la Bolero ,mazungumika ,humbo ndi kasangamala kungotchulapo ochepa. Anthu okhala mmaderawa amavutika ndi mdima amasowa kotcharger mafon, ndi Zina, amayenda mitunda yapafupifupi makilomita 6-8 kuti apeze chigayo ,akamete...