Nditakhala kuti ndapatsidwa nawo mwayi owina 3 million nditha kuyamba ulimi wa Tomato ndi Khumba. Popeza thawi zonse anthu amafuna tomato ndiye nditha kumapezeka ndi tomato chaka chonse. Izi zitha kukhala choncho potengera kuti nditha kuligawa dimba langa ma section osiyanasiyana kuti ndizitha kumalima tomato chaka chonse. Mwachitsazo pamene section ina ndikudzala, section ina akupanga maluwa, section ina akuyamba...