Nditakhala kuti ndapatsidwa nawo mwayi owina 3 million nditha kuyamba ulimi wa Nthochi ndi Zembe. Nditha kugula dimba koguliratu ndikudzalamo nthochi komaso zimbe. Malingana ndikukwera kwa mitengo ya nthochi dziko muno nditakhala kuti ndili ndi hafu ekala dimba lonse lodzadza ndi nthochi za high breed. Nditha kumakolo pafupifupi 1tone pa mwenzi ulionse ndipo ndintha kumagwira ndilama zoposera K700, 000 pa mwenzi uli...