Ndikapatsidwa MK3,000,000 ndidzatsegula sitolo ya FASHION HUB 365. Ndalama zidzagwiritsidwa motere: 1. MK1,900,000 - Kugula zovala zoyambira zabwino and zotchipilako komaso kuonetsetsa kuti kuoda zimene anthu amazinthamangila 2. MK500,000 - Kubwereka sitolo kwa miyezi 3 + kugula ma shelf ndi zida 3. MK200,000 - Kutsatsa pa Facebook/TikTok + kulipira anthu a delivery 4. MK400,000 - Ndalama zosungira zadzidzidzi...