I want to start Fresh Style Clothes & Shoes, a small fashion business that will focus on selling good quality clothes and shoes at affordable prices. Ndidzagulitsa zinthu monga T-shirts, jeans, trousers, shirts, hoodies, dresses, sneakers, sandals ndi ma shoes ena omwe achinyamata amakonda. Business yanga idzakhala ndi physical selling komanso online selling through WhatsApp, Facebook and TikTok. Izi zithandiza kuti...