If I can have 3million light now, choyamba ndipanga kaye budget and list all things that i can have to help me in my business .then where can I do my business (location) kut ngat ndingayiyambe kumeneko zitheka komaso ndima price omwe ndingawapase anthu azibwera.koma chachikulu kwambr it a quality of the things ndingakhale nazo like shop,materials and the smartnes yanga kapena ngat ndikhale ndi munthu wondithandiza...