Choyamba ndikusaka ndalama yosachepera five hundred thousand,kenako kupeza anthu omwe ali ndikuthekela kut angawete ziweto ya nyama ya nkhumba kuti pamapeto azapeze mbweu chiweto chomwe angatenge pakugawana anawo mofanana ndkubweza kholo kwaogula. Kuno kwathu anthu amagulisa ziweto za nyama yankhumba pantengo wa 40 mpaka 50 thousand so pa capital ya k500,000 titha kugula nyama zosachepela 7 pa ntengo wa k50,000...