Ulimi wa nkhuku ndi umodzi mwa ulimi wa ziweto omwe ndi opindulisa ngat ziweto zathu zitasamalidwa bwino .ulimi wu umachita bwino ngati ziweto zathu zikusamalidwa bwino pozipasa zokudya zamagulu monga ma protein ndi Zina zambiri.ulimi wa ziweto monga nkhuku ulipo mitundu iwiri .woyamb ndi ulimi wa nkhuku zanyama komaso ulimi wa nkhuku zamazira.nkhuku zanyama kut zichite bwino zimafunik kupasidwa zokudya zomanga...