Iyi ndi business imene tingamakagule mbeu za ndiwo kwa alimi ndikumagulitsa mdera lathu izi ndi mbeu monga:Nyemba,Soya,Ntedza.iyi ndi business yomwe likatukula mudzi komaso ntedza ndi soya zofunika kumatupi anthu pachifukwa ichi tizapanga kuthekela kuti aliyese azikwanitsa kufikilidwa ndi malondawa kusatengela kutalikilana ndi madera izungulila.business ya mbeu imeneyi timakagula alimi omwe ali ndi mbeu za...