Phone accessories,ndi bussines yokhayo ndakhala ndikuyifuna kumtima kwanga koma chifukwa chosowa capital ndimakanika kuyamb, bussines iyiii ndimawona kuti ikhoza kusitha moyo wanga chifukwa dera lomwe ndili anthu amasowekera kwambiri katundu ameneyo.bussines ya accessories ndimwona kuti ndiyotheka kwambiri