Young Builders Challenge Season 2Agriculture - Idea / Concept
Buy and sell goats _ motani ulimi wa mbudzi ndi ulimi omwe uli wachangu ndi wandalama utakhala uli ndi k3 million utha kudzilemba ntchito wekha pogula mbudzi za 2 million kumadziwetanso wekha kwa chaka chimodzi pokutha chaka chimenecho zizakhala mbudzi zi