ndikupanga bussiness ya butchery koma ndimapangila pa nyumba, chifukwa chakuchepa kwa capital komanso timagwilisa ntchito fridge ya panyumba